Kodi katemera angathandize bwanji kupewa chiwewe cha agalu?

Abstract

Chiwewe ndi nthenda yowopsa kwambiri m'madera ambiri amu Afilika. Ngakhale zili choncho, ndiyopeweka kudzera mu katemera. Katemera amateteza agalu ndikuwakanikitsa kufalitsa matendawa kwa zinyama zina, inde ngakhalenso kwa anthu.

Citation

ILRI. 2023. Kodi katemera angathandize bwanji kupewa chiwewe cha agalu? Video. Nairobi, Kenya: ILRI.

Authors

  • International Livestock Research Institute